Zambian Music 2025Zambian Songs

Kondwa – Siniziba

Kondwa – Siniziba Mp3 Download

Super talented Zambian music singer and songwriter – Kondwa comes through with yet another brand new song tagged “Siniziba“. 

., Download, Listen & Share..

Download Now

Lyrics
“Time
Waits for no one” papa told me
So don’t waste it darling
Umoyo wanga ni olimbikila
Nika ganiza kwamene nachokela
Mutima uma pwanya
Sinifuna kubwelela
Ndiye chifukwa nima yesa
Koma siniziba
Nthawi zina chima lema
Koma siniziba
Nthawi zina sini maziba
Nika yan’gana bonse ba nzanga
Nina yamba nabo
Nima ganiza kapena ni taya nthawi
Vonse nima yesa
Vonse nima chita
Kapena sini chita vokwanila
Koma amai akuti
Mwana wanga vonse vili na nthawi
Uku kuyesa kwamene uyesa pano
Siku taya nthawi upunzila
Koma siniziba
Nthawi zina nima lema
Koma siniziba
Nthawi zina sini maziba
Siniziba kulimba
Siniziba vochita
Siniziba voganiza
Ndine muntu chabe
Ni malema koma osa leka
Uzafika
Baliko bamene sibenzo ziba
Nthawi zina
Bana fika
Nawe uza fika
Lyrics By Alpha
Back to top button