Malawi MusicMalawi On DemandZambian Music 2025

Driemo – Pano Mp3 Download

Driemo – Pano Mp3 Download

Malawian super talented top notch artist who as been trending for sometime now – Driemo who as showed up on the Malawian music scene with a brand new song tagged “Pano“. The brand new song tagged Pano marks as Driemo’s first release this month of January and also marks as his first release this year of 2023. The song Pano is a follow up of Driemo’s previous hit single dubbed “Mojo“.

., Download, Listen & Share..

Download

VERSE ONE

Is this a joke
Are you kidding me

Utanthauza chan
Zachuluka ndi nkhani you’re planning to leave me

Am I a fool
For falling for you
Tadutsa mu zambiri
Tapanga ndi Zambiri
Now you want to switch like dat

PRE HOOK
Kodi ndayipa pano
Ndakubhowa pano
Zonse zija wandichititsa zikayipe pano
Ooh Kodi ndayipa pano
Ndakubhowa pano
Zonse zija unandiphunzitsa zikayipe lero.

HOOK
Unandiyambitsa shisha mowa mesa ndiwe..
Iwe na ine muma club everyday
Lero ukut khalidwe LA banja mwa ine
Kodi ndi game yantundu wanji you’re playing
Nde unkandisinthiranji..
Sinthiranji…
Nde unkandisinthiranji… Oh my God.

VERSE2

Fees yako itashupha ndinagulitsa munda ine..
Lero munagwidwa ndi shasha
Ati ine ndiwakumunda oooh

Koma izizi ndinkapanga chifukwa ndimasamala za iwe
Ineyo ndinkablunder kufuna kukusangalatsa iwe

How I wish I could go back
How I wish I could rewind
How I wish I could fall back
But it’s too late
Too late

PRE HOOK
Kodi ndayipa pano
Ndakubhowa pano
Zonse zija unandiphunzitsa zikayipe lero

HOOK
Unandiyambitsa shisha mowa mesa ndiwe..
Iwe na ine muma club everyday
Lero ukut khalidwe LA banja mwa ine
Kodi ndi game yantundu wanji you’re playing
Nde unkandisinthiranji..
Sinthiranji
Nde unkandisinthiranjiii
Oh my God

BRIDGE
Zomwe mutandi siyire pano
Ndizomwe mudandiphunzitsa
Zomwe mutanditukwane nazo pano
Ndizomwe mudandidziwitsaaa iiiiiiineeeeeee.

Lyrics By Alpha

Content Tags

Driemo – Pano

Driemo – Pano Mp3 Download

Download Driemo – Pano Mp3 

Driemo – Pano Lyrics 

Back to top button