Videos

Goddy Zambia ft. Macky 2 – Inu Mayi (Offcial Video)

Super talented singer – Goddy Zambia drops the visuals of his hit single tagged “Inu MayI which is a song taken off from his album “Underrated“. The music video was directed by The Epic Director Chichi Ice (Tip Tronic Media Arts) & Director Blue.

Watch The Video Below!!

LYRICS: Inu mayi Kodi mulikumva ?ah Ndingaseke njila Zina koma kunsi ndima sowa Inu Inu mayi Kodi mukumbukira Kuti muli ndi Ana mwina munati iwalako (Inu mayi ,Inu mama kodziko la amalemu uko Ah ah ah ah inu mayi mugone mu mtendere Inu mama) VERSE (Goddy) Kodi mumadya zichani Kuvala zichani Kodi nyumba mukhalamo yo Anamanga ndani Pomwe munafa anakulandilani ndi ndani Mafunso ndi wambiri pa tisakulise nkhani Leka ndi kambe ndi yesu ambuye wanga ndinu Munawadziwa mayi anga asanakhale malemu Mwina anali muntu ochimwa pa maso panu Koma kumulanda moyo chinapweteketsa khamu Kodi munalowa m’jerusalema ? Mwina munalowako kugahena Kodi munaonana namalenga Mwinanu munango werudzika Munali ndi Ana achichepere ×2 (kudziko munasiya mayi anga? CHORUS: Inu mayi Kodi mulikumva ?ah Ndingaseke njila Zina koma kunsi ndima sowa Inu Inu mayi Kodi mukumbukira Kuti muli ndi Ana mwina munati iwalako (Inu mayi ,Inu mama kodziko la amalemu uko Ah ah ah ah inu mayi mugone mu mtendere Inu mama) VERSE : (Macky 2) Uko kumwamba kwemulili mulungu amisunge, Apitilize chingiliza devil asanitunke Ma letter nimamilembela ninshi siyana fike Ndaba mafunso ninafunsa neo simunayanke Nikali funo ziba why munanisiya so? Tinaluvyanya chani ndaba we reap what we sow? They say celebrate life when somebody dies, but when we think of you everybody cries Dear mama! Dear mama! I can’t wait for the day yene tizakakumana. They told me limba mwamuna samalila, but chikonko mutima chaugwililila. Everything I have is all because of you, so it’s only right I sing this song for you, and if all this money can’t even bring me joy then at least let me be a Mama’s boy.

 

 

Back to top button